podcasts.eu.org

TTB Chichewa Phunziro la Baibulo (Chichewa)

by THRU the BIBLE · 1,000 episodes

ReligionSpiritualityChristianity

Website ↗ More by author

Dziwani Mawu onse a Mulungu kudzera mu maphunziro odalirika a Baibulo a THRU the BIBLE m’Chichewa. Gawo lililonse limapereka chiphunzitso chomveka komanso chothandiza kuti mumvetse Malemba ndi kuwagwiritsa ntchito pa moyo wa tsiku ndi tsiku. Yendani m’Baibulo phunziro limodzi pa nthawi limodzi ndi omvera padziko lonse. Dziwani zambiri pa TTB.BIBLE

Latest episodes

  1. Chilango cheni-cheni cha Israyeli

  2. Israyeli abwerera ku mafano ya ana ang’ombe ndi ku maguwa a Uchimo

  3. Israyeli atembenukira ku Aigupto ndi Assyria

  4. Israyeli ali ndi mwayi wobwereranso kwa Mulungu pachilango chatsopano

  5. Israyeli achoka pamaso pa Mulungu ndipo Mulungu achokanso kwa iye

  6. Uchimo wa Israyeli ndi wa ife tonse

  7. Uchimo wa Israyeli pamaso pa Mulungu

  8. Kufotokonzera tchimo la Israyeli

  9. Mulungu alowetsa Israyeli mupangano lake

  10. Gomeri ndi Israyeli aonetsa kusakhulupirika pamene Mulungu ndiye wokhulupirika

  11. Ukwati wa Hoseya ndi Gomeri, mkazi wachiwerewere

  12. Kuonetsa moyo wa Hoseya ndi aneneri ena ang’ono

  13. Mau otsogolera a chiwiri- kusweka mtima kwa Mulungu

  14. Moyo wauzimu wa wokhulupirira

  15. Momwe wokhulupirira angakhalire ndi anthu ena

  16. Kuopsa kochoka pamaso pa Kristu mwachisinsi m’moyo wa mkristu

  17. Tsoka pakuchotsa maso pa Ambuye Yesu Kristu ndi kuika pamunthu

  18. Wokhulupirira ali pampikisano ndi pankhondo ndi satana

  19. Moyo wa mkristu uli pampikisanokomanso kulimbana ndisatana.

  20. Ulendowa mkristu

    Ulendo wa Mkhristu mu chikhulupiriro

Nothing playing
0:00 / 0:00